- Anglický jazyk
Nditha Kuwerenga Baibulo Langa
Autor: Kathy Sheppard
Thandizani ana anu kukhala odzidalira powerenga okha Baibulo Aloreni kuwerenga okha nkhani zosangalatsa zosiyanasiyana za m'baibulo pa nthawi imene akufuna kutero. Mwakutero, adzakhala ndi lusa lomvetsa zinthu pawokha mwachangu ndi kuzigwilitsa bwino ntchito... Viac o knihe
Na objednávku
16.90 €
bežná cena: 19.20 €
O knihe
Thandizani ana anu kukhala odzidalira powerenga okha Baibulo Aloreni kuwerenga okha nkhani zosangalatsa zosiyanasiyana za m'baibulo pa nthawi imene akufuna kutero. Mwakutero, adzakhala ndi lusa lomvetsa zinthu pawokha mwachangu ndi kuzigwilitsa bwino ntchito chomwe ndi chuma chokhazikika. Lolani kuti, chikondi cha Mulungu chomwe ndi chopanda malire, chiwalire pa miyoyo ya ana anu.
- Vydavateľstvo: Lulu.com
- Rok vydania: 2012
- Formát: Paperback
- Rozmer: 280 x 216 mm
- Jazyk: Anglický jazyk
- ISBN: 9781291113198